Numbers 2:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amange pafupi ndi fuko lake akhale a fuko la Simeoni, limene mtsogoleri wake ndi Selumiele mwana wa Zurishadai,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Simeoni; ndi kalonga wa ana a Simeoni ndiye Selumiele mwana wa Zurishadai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Fuko la Simeoni lidzamanga pafupi ndi Rubeni. Mtsogoleri wa gulu la Simeoni ndi Selumieli mwana wa Zurisadai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a pfuko la Simeoni; ndi kalonga wa ana a Simeoni ndiye Selumiyeli mwana wa Surisadai.