Numbers 2:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pabwere fuko la Gadi, limene mtsogoleri wake ndi Eliyasafu, mwana wa Deuwele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi fuko la Gadi; kalonga wa ana a Gadi ndiye Eliyasafu mwana wa Reuwele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lotsatira lidzakhala fuko la Gadi. Mtsogoleri wa gulu la Gadi ndi Eliyasafu mwana wa Deuweli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pfuko la Gadi; kalonga wa ana a Gadi ndiye Eliyasafe mwana wa Reueli.