Numbers 2:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo ankhondo ake ngokwanira 45,650.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 45,650.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi khamu lace, ndi owerengedwa ace, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu.