Numbers 2:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amange pafupi ndi fuko lake akhale a fuko la Manase, limene mtsogoleri wake ndi Gamaliele mwana wa Pedazuri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo oyandikizana naye ndiwo a fuko la Manase; ndi kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliele mwana wa Pedazuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Fuko la Manase lidzakhala pafupi ndi Efereimu. Mtsogoleri wa Amanase ndi Gamalieli mwana wa Pedazuri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo oyandikizana naye ndiwo a pfuko la Manase; ndi kalonga wa ana a Manase ndiye Gamaliyeli mwana wa Pedazuri.