Numbers 2:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pabwere fuko la Benjamini, limene mtsogoleri wake ndi Abidani mwana wa Gideoni,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi fuko la Benjamini: kalonga wa ana a Benjamini ndiye Abidani mwana wa Gideoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lotsatira lidzakhala fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa Abenjamini ndi Abidani mwana wa Gideoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pfuko la Benjamini: kalonga wa ana a Benjamini ndiye Abidana mwana wa Gideoni.