Numbers 2:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pabwere fuko la Nafutali, limene mtsogoleri wake ndi Ahira mwana wa Enani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi fuko la Nafutali: ndi kalonga wa ana a Nafutali ndiye Ahira mwana wa Enani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lotsatira lidzakhala fuko la Nafutali. Mtsogoleri wa Anafutali ndi Ahira mwana wa Enani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pfuko la Nafitali: ndi kalonga wa ana a Nafitali ndiye Ahira mwana wa Enani.