Numbers 2:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Alevi sadaŵaŵerengere kumodzi ndi Aisraele, monga momwe Chauta adaalamulira Mose.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sanawerenge Alevi mwa ana a Israele; monga Yehova adauza Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Alevi sanawawerenge pamodzi ndi Aisraeli enawo monga momwe Yehova analamulira Mose.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sanawerenga Alevi mwa ana a Israyeli; monga Yehova adauza Mose.