Numbers 20:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Mose ndi Aroni adasonkhanitsa mpingo wonse pamodzi kuthanthweko nauza anthuwo kuti, “Imvani anthu opandukanu. Kodi tichite kukutulutsirani madzi m'thanthwemu?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose ndi Aroni anasonkhanitsa msonkhano pathanthwe, nanena nao iye, Tamvanitu, opikisana naye inu; kodi tikutulutsireni madzi m'thanthwe umu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose ndi Aaroni anasonkhanitsa anthuwo pamodzi ku thanthwelo ndipo Mose anawawuza kuti, “Tamverani osamvera inu, kodi tikupatseni madzi kuchokera ku thanthwe ili?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose ndi Aroni anasonkhanitsa msonkhano pathanthwe, nanena nao iye, Tamvanitu, opikisana naye inu; kodi tikuturutsireni madzi m'thanthwe umu?