Numbers 20:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu makolo athu adaapita ku Ejipito, ndipo tidakhala kumeneko zaka zambiri. Aejipito adatizunza ife ndi makolo athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti makolo athu anatsikira kunka ku Ejipito, ndipo tinakhala m'Ejipito masiku ambiri; ndipo Aejipito anachitira zoipa ife, ndi makolo athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makolo athu anapita ku Igupto ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri. Aigupto anatizunza pamodzi ndi makolo athuwo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti makolo athu anatsikira kumka ku Aigupto, ndipo tinakhala m'Aigupto masiku ambiri; ndipo Aaigupto anacitira zoipa ife, ndi makolo athu.