Numbers 20:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Edomu adayankha kuti, “Musadzere kuno, kuti ndingafike kudzakubayani ndi lupanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Edomu ananena naye, Usapitire pakati pa ine, kuti ndingatuluke kukomana nawe ndi lupanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Edomu anayankha kuti, “Musadutse kuno: Mukangoyesera tidzabwera ndi kumenyana nanu ndi lupanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Edomu ananena naye, Usapitire pakati pa ine, kuti ndingaturuke kukomana nawe ndi lupanga.