Numbers 20:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Edomu sadavomere kuti Aisraele adutse m'dziko mwake. Ndipo Aisraele adadzera njira ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero Edomu anakana kulola Israele kupitira pa malire ake; chifukwa chake Aisraele anampatukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Edomu anakaniza Israeli kuti adutse mʼdziko lake, choncho Israeli anabwerera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero Edomu anakana kulola Israyeli kupitira pa malire ace; cifukwa cace Aisrayeli anampatukira.