Numbers 20:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko umvule Aroni zovala zaunsembe ndi kuveka mwana wake Eleazara. Ndipo Aroni adzafera komweko.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nuvule Aroni zovala zake, numveke Eleazara mwana wake; ndipo Aroni adzaitanidwa kunka kwa anthu a mtundu wake, nadzafa komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uvule Aaroni zovala zake ndipo umuveke mwana wake Eliezara, pakuti Aaroni adzafera komweko, ndipo adzakakhala ndi anthu a mtundu wake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nubvule Aroni zobvala zace, numbveke Eleazara mwana wace; ndipo Aroni adzaitanidwa kumka kwa anthu a mtundu wace, nadzafa komweko.