Numbers 21:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake buku la nkhondo za Chauta limanena kuti, “Mzinda wa Waheba uli ku Sufa, ku zigwa za Arinoni,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake, ananena m'buku la Nkhondo za Yehova, Waheba m'Sufa, ndi miyendo ya Arinoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake Buku la Nkhondo za Yehova limati, “Mzinda wa Wahebu uli mu Sufa, mu zigwa za Arinoni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace, ananena m'buku la Nkhondo za Yehova, Vahebi m'Sufa, Ndi miyendo ya Arinoni;