Numbers 21:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ku matsitso a zigwa amene afika mpaka ku Ari, nakhudza malire a dziko la Mowabu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zigwa za miyendoyo zakutsikira kwao kwa Ari, ndi kuyandikizana ndi malire a Mowabu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ku matsitso a zigwa amene afika mpaka ku Ari nakhudza malire a dziko la Mowabu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi zigwa za miyendoyo Zakutsikira kwao kwa Ari, Ndi kuyandikizana ndi malire a Moabu.