Numbers 21:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake oimba ndakatulo amati, “Bwerani ku Hesiboni, mzindawu umangidwenso, tiyeni timange mzinda wa Sihoni kuti ukhazikikenso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake iwo akunena mophiphiritsa akuti, Idzani ku Hesiboni, mudzi wa Sihoni umangike, nukhazikike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake alakatuli amati: “Bwerani ku Hesiboni, mzindawo umangidwenso; mzinda wa Sihoni ukhazikike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace iwo akunena mophiphiritsa akuti, Idzani ku Hesiboni, Mudzi wa Sihoni umangike, nukhazikike: