Numbers 21:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa iwe Mowabu, mwatha inu anthu opembedza Kemosi. Ana ake aamuna waasandutsa othaŵathaŵa, ana ake aakazi waasandutsa akapolo, akapolo a Sihoni mfumu ya Aamori.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka kwa iwe, Mowabu! Mwaonongeka, anthu a Kemosi inu, anapereka ana ake amuna opulumuka, ndi ana ake akazi akhale ansinga, kwa Sihoni mfumu ya Aamori.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka kwa iwe Mowabu! Mwawonongedwa inu anthu a ku Kemosi! Ana ake aamuna wawasandutsa ngati anthu othawathawa ndipo ana ake aakazi ngati akapolo, akapolo a Sihoni, mfumu ya Aamori.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka kwa iwe, Moabu! Mwaonongeka, anthu a Kemosi inu, Anapereka ana ace amuna opulumuka, Ndi ana ace akazi akhale ansinga, Kwa Sihoni mfumu ya Aamori.