Numbers 22:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Balamu adayankha kuti, “Balaki mwana wa Zipora mfumu ya Mowabu, watumiza uthenga kudzandiwuza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Balamu anati kwa Mulungu, Balaki mwana wa Zipori mfumu ya Mowabu, anatumiza kwa ine, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Balaamu anayankha Mulungu kuti, “Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananditumizira uthenga uwu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Balamu anati kwa Mulungu, Balaki mwana wa Zipori mfumu ya Moabu, anatumiza kwa ine, ndi kuti,