Numbers 22:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Balaki adatumanso akalonga ochuluka ndi olemekezeka kopambana oyamba aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Balaki anaonjeza kutumanso akalonga, ochuluka, ndi omveka koposa awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Balaki anatumanso akuluakulu ena ambiri ndi olemekezeka kwambiri kuposa oyamba aja ndipo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Balaki anaonjeza kutumanso akalonga, ocuruka, ndi omveka koposa awa.