Numbers 22:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adafika kwa Balamu namuuza kuti, “Balaki mwana wa Zipora akunena kuti, ‘Musalole kuti chinthu chilichonse chikuletseni kubwera kwa ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza kwa Balamu, nati kwa iye, Atero Balaki mwana wa Zipori, Pasakhaletu chinthu chakukuletsa kudza kwa ine;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anafika kwa Balaamu nati; “Zomwe Balaki mwana wa Zipori akunena ndi izi: ‘Usalole kuti china chilichonse chikulepheretse kubwera kwa ine,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza kwa Balamu, nati kwa iye, Atero Balaki mwana wa Zipori, Pasakhaletu cinthu cakukuletsa kudza kwa ine;