Numbers 22:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye inu tsono, gonani konkuno usiku uno, monga adachitira anzanu aja, kuti ndidziŵe ngati pali zina zimene Chauta andiwuze.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikupemphani, tsono, khalani pano inu usiku uno womwe; kuti ndidziwe chomwe Yehova adzanenanso nane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano mukhale kuno usiku uno monga ena anachitira, ndidzaona chimene Yehova adzandiwuza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikupemphani, tsono, khalani pano inu usiku uno womwe; kuti ndidziwe comwe Yehova adzanenanso nane.