Numbers 22:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Balamu adayankha mngelo wa Chauta uja kuti, “Ndachimwa. Sindinalikudziŵa kuti mukunditsekera njira. Nchifukwa chake tsono, ngati zakuipirani, ndibwerera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Balamu anati kwa mthenga wa Yehova, Ndachimwa, popeza sindinadziwa kuti munaima mondiletsa m'njira; ndipo tsopano, ngati chikuipirani, ndibwerera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Balaamu anati kwa mngelo wa Yehova uja, “Ndachimwa. Sindinadziwe kuti munayima pa njira kunditsutsa. Tsopano ngati Inu simunakondwe, ineyo ndibwerera.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Balamu anati kwa mthenga wa Yehova, Ndacimwa, popeza sindinadziwa kuti munaima mondiletsa m'njira; ndipo tsopano, ngati cikuipirani, ndibwerera.