Numbers 22:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Balamu adayankha Balaki kuti, “Inde, ndabwera, koma kodi ndili ndi mphamvu zoti ndilankhule chinthu chilichonse? Ndiyenera kulankhula zokhazo zimene Mulungu andiwuze.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndili nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? Mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Balaamu anayankha Balaki kuti, “Taonani, ndabwera kwa inu lero, kodi ine ndili ndi mphamvu zoti nʼkuyankhula chilichonse? Inetu ndiyenera kuyankhula zokhazo zimene Mulungu wandiwuza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndiri nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena.