Numbers 22:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake Balaki adatenga Balamu, napita naye ku mapiri a Bamoti-Baala, kumene Balamuyo ankatha kuwona mahema onse a Aisraele mpaka ku mathero ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali kuti m'mawa, Balaki anatenga Balamu, nakwera naye ku misanje ya Baala, ndi kumeneko anaona malekezero a anthuwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake Balaki anatenga Balaamu napita limodzi ku Bamoti Baala, ndipo kumeneko anakaonako gulu lina la Aisraeliwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali kuti m'mawa, Balaki anatenga Balamu, nakwera nave ku misanje ya Baala, ndi kumeneko anaona malekezero a anthuwo.