Numbers 23:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adayankha kuti, “Kodi sindiyenera kulankhula zokhazo zimene Chauta adaika m'kamwa mwanga?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayankha nati, Chimene achiika m'kamwa mwanga Yehova, sindiyenera kodi kunena ichi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankha kuti, “Kodi sindinayenera kuyankhula zimene Yehova anandiwuza?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayankha nati, Cimene aciika m'kamwa mwanga Yehova, sindiyenera kodi kunena ici?