Numbers 23:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Balamu adauza Balaki kuti, “Imani pano pafupi ndi nsembe yanu yopsereza, ine ndipite ndikakumane ndi Chauta apo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa Balaki, Imani pano pa nsembe yopsereza yanu, ndipite ine ndikakomane ndi Iye uko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Balaamu anawuza Balaki kuti, “Khalani pano pafupi ndi nsembe yanu pamene ine ndikukakumana ndi Mulungu cha uko.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa Balaki, Imani pano pa nsembe yopsereza yanu, ndipite ine ndikakomane ndi iye uko.