Numbers 23:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Balamu adayamba kulankhula mau auneneri, adati, “Dzukani, Balaki, ndipo mumve, mundimvere inu mwana wa Zipori.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ukani, Balaki, imvani; ndimvereni, mwana wa Zipori.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Balaamu ananena uthenga wake: “Nyamuka Balaki ndipo tamvera; Undimvere iwe mwana wa Zipori.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena fanizo lace, nati, Ukani, Balaki, imvani; Ndimvereni, mwana wa Zipori;