Numbers 23:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adaŵatulutsa m'dziko la Ejipito, ali ndi mphamvu zonga za njati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu awatulutsa m'Ejipito; mphamvu yake ikunga ya njati.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wowatulutsa mʼdziko la Igupto, ali ndi mphamvu ngati za njati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu awaturutsa m'Aigupto; Mphamvu yace ikunga ya njati.