Numbers 23:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Balamu adafunsa Balakiyo kuti, “Kodi sindidakuuzeni kuti ndiyenera kuchita zonse zimene Chauta wandiwuza?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Balamu anayankha nati kwa Balaki, Sindinakuuzani ndi kuti, Chilichonse achinena Yehova, chomwecho ndizichita?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Balaamu anayankha Balaki kuti, ‘Kodi sindinakuwuzeni kuti ndiyenera kuchita zimene Yehova wanena?’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Balamu anayankha nati kwa Balaki, Sindinakuuzani ndi kuti, Ciri conse acinena Yehova, comweco ndizicita?