Numbers 23:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adauza Balamu kuti “Bwerera kwa Balaki, ukamuuze izi! Izi”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anaika mau m'kamwa mwa Balamu, nati, Bwerera kwa Balaki, nukanene chakutichakuti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anawuza Balaamu kuti, “Bwerera kwa Balaki ndipo ukamuwuze uthenga uwu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anaika mau m'kamwa mwa Balamu, nati, Bwerera kwa Balaki, nukanene cakuti cakuti.