Numbers 23:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndikuŵaona kuchokera pamwamba pa phiri, pamene ndikuŵayang'ana kuchokera ku mapiri, ndikuwona anthu okhala paokha, osadziŵerengera kumodzi ndi mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, pokhala pamwamba pa matanthwe ndimpenya, pokhala pa zitunda ndimuyang'ana; taonani, ndiwo anthu akukhala pa okha. Osadziwerengera pakati pa amitundu ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera pamwamba pa mapiri ndikuona anthu, ndikuwaona kuchokera pa zitunda. Ndikuona anthu okhala pawokha, osakhala mʼgulu limodzi ndi mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, pokhala pamwamba pa matanthwe ndimpenya, Pokhala pa zitunda ndimuyang'ana; Taonani, ndiwo anthu akukhala paokha. Osadziwerengera pakati pa amitundu ena,