Numbers 24:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake, chokani, kazipitani kwanu. Ndidaakuuzani kuti ndidzakupatsani mphotho, koma Chauta wakana kuti muilandire mphothoyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake thawira ku malo ako tsopano; ndikadakuchitira ulemu waukulu; koma, taona, Yehova wakuletsera ulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano choka msanga uzipita kwanu! Ndinanena kuti ndidzakulipira bwino kwambiri, koma Yehova sanafune kuti ulandire malipirowo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace thawira ku malo ako tsopano; ndikadakucitira ulemu waukuru; koma, taona, Yehova wakuletsera ulemu.