Numbers 24:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Balamu adauza Balaki kuti, “Tsopano ndikupita kwa anthu anga. Bwerani kuno, ndikudziŵitseni zimene Aisraeleŵa adzaŵachite anthu anu masiku akudzaŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano, taonani, ndimuka kwa anthu a mtundu wanga; tiyeni, ndidzakulangizani, ndi kukuuzani zimene anthu awa adzachitira anthu anu, masiku otsiriza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano ndikupita kwa anthu anga, koma tabwerani ndikuchenjezeni zimene anthu awa adzachitira anthu anu masiku akubwerawa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano, taonani, ndimuka kwa anthu a mtundu wanga; tiyeni, ndidzakulangizani, ndi kukuuzani zimene anthu awa adzacitira anthu anu, masiku otsiriza.