Numbers 24:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko la Edomu lidzalandidwa, Seiri mdani wake adzagonjetsedwa, pamene Aisraele adzakhala akupambanabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Edomu adzakhala akeake, Seiri lomwe lidzakhala lakelake, ndiwo adani ake; koma Israele adzachita zamphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Edomu adzagonjetsedwa; Seiri, mdani wake, adzawonongedwa koma mphamvu za Israeli zidzachuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Edomu adzakhala ace ace, Seiri lomwe lidzakhala lace lace, ndiwo adani ace;