Numbers 24:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa Yakobe mudzatuluka mfumu yolamulira, imene idzaononga otsala mu mzinda.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wina wotuluka m'Yakobo adzachita ufumu; nadzapasula otsalira m'mudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wolamulira adzachokera mwa Yakobo ndipo adzawononga otsala a mu mzindamo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Israyeli adzacita zamphamvu. Ndipo wina woturuka m'Yakobo adzacita ufumu; Nadzapasula otsalira m'mudzi.