Numbers 24:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaona Aisraele ali m'mahema mwao, fuko lililonse pa lokha. Tsono mzimu wa Mulungu udatsika pa iye,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Balamu anakweza maso ake, naona Israele alikukhala monga mwa mafuko ao; ndipo mzimu wa Mulungu unadza pa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Balaamu atayangʼana, anaona Aisraeli atamanga misasa yawo fuko ndi fuko. Pamenepo mzimu wa Mulungu unabwera pa iye
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Balamu anakweza maso ace, naona Israyeli alikukhala monga mwa mafuko ao; ndipo mzimu wa Mulungu unadza pa iye.