Numbers 24:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adayamba kulankhulanso nati, “Kalanga ine, ndani akhale moyo, Mulungu akachita zimenezi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ha! Adzakhala ndi moyo ndani pakuchita ichi Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ananenanso uthenga wina kuti, “Aa, ndani adzakhala ndi moyo Mulungu akachita zimenezi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena fanizo lace, nati, Ha! adzakhala ndi moyo ndani pakucita ici Mulungu?