Numbers 24:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo adayamba kulankhula mau auneneri, adati, “Mau a Balamu mwana wa Beori, mau a munthu amene maso ake ndi otsekuka,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ananena fanizo lake, nati, Balamu mwana wa Beori anenetsa, ndi munthuyo anatsinzina maso anenetsa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ananena uthenga wake: “Uthenga wa Balaamu mwana wa Beori, uthenga wa amene diso lake ndi lotsekuka,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ananena fanizo lace, nati, Balamu mwana wa Beori anenetsa, Ndi munthuyo anatsinzina maso anenetsa;