Numbers 24:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
munthu amene akumva mau a Mulungu, munthu amene akuwona Mphambe m'masomphenya, munthu amene akugwa pansi, koma maso ali chipenyere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anenetsa wakumva mau a Mulungu, wakuona masomphenya a Wamphamvuyonse, wakugwa pansi maso ake openyuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
uthenga wa amene amamva mawu a Mulungu, yemwe amaona masomphenya wochokera kwa Wamphamvuzonse, yemwe amagwa chafufumimba, koma maso ake ali chipenyere:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wakumva mau a Mulungu anenetsa, Wakuona masomphenya a Wamphamvuyonse, Wakugwa pansi maso ace openyuka: