Numbers 24:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ako ali ngati zigwa zofika patali, ali ngati minda ya m'mbali mwa mtsinje, ali ngati khonje amene Chauta adabzala, ali ngati mitengo ya mkungudza yomera m'mbali mwa madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ziyalika monga zigwa, monga minda m'mphepete mwa nyanja, monga khonje wooka Yehova, monga mikungudza m'mphepete mwa madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Monga zigwa zotambalala, monga minda mʼmbali mwa mtsinje, monga aloe wodzalidwa ndi Yehova, monga mikungudza mʼmbali mwa madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ziyalika monga zigwa, Monga minda m'mphepete mwanyanja, Monga khonje waoka Yehova, Monga mikungudza m'mphepete mwa madzi.