Numbers 26:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Utatha mliriwo, Chauta adauza Mose ndi Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Utatha mliri Yehova anati kwa Mose ndi Eliezara mwana wa Aaroni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati,