Numbers 26:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo nthaka idang'ambika ndi kuŵameza onsewo pamodzi ndi Kora, kotero kuti gulu lao lidafa pamene moto udapsereza anthu 250 aja, nasanduka chenjezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo dziko linayasama pakamwa pake, ndi kuwameza pamodzi ndi Kora, pakufa msonkhano uja; muja moto unaononga amuna mazana awiri ndi makumi asanu, nakhala iwo chizindikiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthaka inangʼambika ndi kuwameza pamodzi ndi Kora, kotero kuti gulu lawo linafa pamene moto unapsereza anthu 250 aja, nasanduka chenjezo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo dziko linayasama pakamwa pace, ndi kuwameza pamodzi ndi Kora, pakufa msonkhano uja; muja mote unaononga amuna mazana awiri ndi makumi asanu, nakhala iwo cizindikilo.