Numbers 26:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa, anthu okwanira 22,200, ndiwo a m'mabanja a Simeoni, amene adaŵerengedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo mabanja a Asimeoni, zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana ziwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa anali mafuko a Simeoni. Iwowa analipo amuna 22,200.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo mabanja a Asimeoni, zikwi makumi awiri mphambu ziwirikudzamazana awiri.