Numbers 26:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsata mabanja ao ana aamuna a Gadi anali aŵa: Zefoni anali kholo la banja la Azefoni. Hagi anali kholo la banja la Ahagi. Suni anali kholo la banja la Asuni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Gadi monga mwa mabanja ao ndiwo: Zefoni, ndiye kholo la banja la Azefoni; Hagi, ndiye kholo la banja la Ahagi; Suni, ndiye kholo la banja la Suni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Gadi mwa mafuko awo ndi izi: kuchokera mwa Zefoni, fuko la Azefoni; kuchokera mwa Hagi, fuko la Ahagi; kuchokera mwa Suni, fuko la Asuni;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Gadi monga mwa mabanja ao ndiwo: Zefoni, ndiye kholo la banja la Azefoni; Hagi, ndiye kholo la banja la Ahagi; Suni, ndiye kholo la banja la Asuni;