Numbers 26:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana aamuna a Yuda anali Ere ndi Onani, koma iwowo adafera m'dziko la Kanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Yuda, ndiwo Eri ndi Onani; ndipo Eri ndi Onani anamwalira m'dziko la Kanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Eri ndi Onani anali ana aamuna a Yuda, koma anafera mu Kanaani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Yuda, ndiwo Eri ndi Onani; ndipo Eri ndi Onani anamwalira m'dziko la Kanani.