Numbers 26:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsata mabanja ao ana aamuna a Isakara anali aŵa: Tola anali kholo la banja la Atola. Puva anali kholo la banja la Apuva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Isakara monga mwa mabanja ao ndiwo: Tola, ndiye kholo la banja la Atola; Puva, ndiye kholo la banja la Apuni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Isakara monga mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Tola, fuko la Atola; kuchokera mwa Puwa, fuko la Apuwa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Isakara monga mwa mabanja ao ndiwo: Tola, ndiye kholo la banja la Atola; Puva, ndiye kholo la banja la Apuni;