Numbers 26:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa, anthu okwanira 64,300, ndiwo anali a m'mabanja a Isakara, amene adaŵerengedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndi amene anali a fuko la Isakara. Amene anawerengedwa analipo 64,300.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu.