Numbers 26:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ameneŵa, anthu okwanira 60,500, ndiwo anali a m'mabanja a Zebuloni, amene adaŵerengedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo mabanja a Zebuloni monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu mazana asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndiwo anali mafuko a Zebuloni. Amene anawerengedwa analipo 60,500.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo mabanja a Zebuloni monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu mazana asanu.