Numbers 26:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Zelofehadi mwana wa Hefere analibe ana aamuna, koma ana aakazi okhaokha. Ana aakazi a Zelofehadi anali aŵa: Mala, Nowa, Hogola, Milika ndi Tiriza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Zelofehadi mwana wa Hefere analibe ana amuna, koma ana akazi ndiwo; ndipo maina a ana akazi a Tselofekadi ndiwo Mala ndi Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Zelofehadi mwana wa Heferi analibe ana aamuna koma ana aakazi okha, amene mayina awo anali: Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.)
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Tselofekadi mwana wa Heferi analibe ana amuna, koma ana akazi ndiwo; ndipo maina a ana akazi a Tselofekadi ndiwo Mala ndi Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.