Numbers 26:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsata mabanja ao ana aamuna a Efuremu anali aŵa: Sutela anali kholo la banja la Asutela, Bekeri anali kholo la banja la Abekeri. Tahani anali kholo la banja la Atahani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana amuna a Efuremu monga mwa mabanja ao ndiwo: Sutela, ndiye kholo la banja la Asutela; Bekere, ndiye kholo la banja la Abekere; Tahani, ndiye kholo la banja la Atahani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Efereimu monga mwa mafuko awo zinali izi; kuchokera mwa Sutela, fuko la Asutela; kuchokera mwa Bekeri, fuko la Abekeri; kuchokera mwa Tahani, fuko la Atahani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana amuna a Efraimu monga mwa mabanja ao ndiwo: Sutela, ndiye kholo la banja la Asutela; Bekeri, ndiye kholo la banja la Abekeri; Tahana, ndiye kholo la banja la Atahana.