Numbers 26:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo ana aamuna a Sutela anali aŵa: Erani anali kholo la banja la Aerani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwana wamwamuna wa Sutela ndiye Erani, ndiye kholo la banja la Aerani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Sutela zinali izi: kuchokera mwa Erani, fuko la Aerani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwana wamwamuna wa Sutela ndiye Erani, ndiye kholo la banja la Aerani.